Mawu a M'munsi
b Baibulo sililetsa kumwa mowa pang’ono. (Salimo 104:15; 1 Timoteyo 5:23) Komabe, limaletsa kumwa mowawo mopitirira malire komanso kuledzera.—1 Akorinto 6:9, 10; Tito 2:3.