Mawu a M'munsi
a James anabadwa m’chaka cha 1566 ndipo anasankhidwa kukhala Mfumu James yanambala 6 ya ku Scotland m’chaka chotsatira. M’chaka cha 1603 anasankhidwa kukhala Mfumu James Yoyamba ya ku England ndipo anayamba kulamulira mayiko onse awiri. Ndipo m’chaka cha 1604, mfumuyi inayamba kudziwika ndi dzina lakuti “Mfumu James ya ku Britain.”