Mawu a M'munsi
a Akatswiri a ku Girisi anali atatulukira kale kuti dziko lapansi ndi lozungulira. Komabe iwo ankadabwa kuti n’chifukwa chiyani nyenyezi inayake yotchedwa North Star imaoneka m’munsi mwa thambo munthu akamalowera chakumpoto.