Mawu a M'munsi
c Werengani 1 Mbiri 1:27-34; 2:1-15; 3:1-24. Pamene Rehobowamu, yemwe anali mwana wa Mfumu Solomo, ankalamulira, mtundu wa Isiraeli unagawanika n’kukhala maufumu awiri, wina unali kumpoto ndipo wina unali kum’mwera. Kuyambira nthawi imeneyo, mtundu wa Isiraeli unkalamuliridwa ndi mafumu awiri pa nthawi imodzi.—1 Mafumu 12:1-24.