Mawu a M'munsi c Padziko lonse, ntchito ya Mboni za Yehova imayendetsedwa ndi ndalama zimene anthu amapereka mwakufuna kwawo.