Mawu a M'munsi a Pali mpukutu umodzi wokha womwe uli ndi buku lonse la Yesaya. Mipukutu inayo ili ndi tizidutswa chabe ta bukuli.