Mawu a M'munsi
a Masiku anonso kuli anthu amakhalidwe abwino amene mungatengere chitsanzo chawo. Anthu amenewa akhoza kukhala makolo, achibale kapena Akhristu anzanu omwe amakonda kwambiri Mulungu. Mukhozanso kutengera chitsanzo cha m’bale kapena mlongo wamakhalidwe abwino amene mukumudziwa kapena amene munawerengapo nkhani yake.