Mawu a M'munsi
b Mukhozanso kuyamba ndi kusankha munthu amene mumamusirira. Mukamusankha dzifunseni kuti, ‘Kodi munthuyu ali ndi khalidwe liti limene ndimafuna nditakhala nalo?’ Kenako, yesetsani kutengera khalidwelo.