Mawu a M'munsi
b Magazini ina inanena kuti ngakhale kuti zakudya monga bowa, nyemba, mphodza, nsawawa, spinachi ndi ndiwo zina zamasamba zili ndi michere yambiri imene ingayambitse nyamakazi ya m’mafupa, “palibe umboni wosonyeza kuti zakudyazi zimayambitsadi matendawa.”