Mawu a M'munsi
c Cholinga cha nkhani ino sikusankhira anthu zochita pa nkhani ya mankhwala. Aliyense ayenera kulandira chithandizo cha mankhwala mogwirizana ndi vuto lake. Choncho simuyenera kusiya kumwa mankhwala amene adokotala anakupatsani kapena kusintha zakudya zimene mumadya musanakambirane ndi adokotala.