Mawu a M'munsi
b Magazini ya Galamukani! sisankhira anthu zochita pa nkhani ya zakudya. Aliyense ayenera kusankha yekha zakudya zoti azidya komanso angafunse adokotala zakudya zimene ayenera kudya. Pewani kumangodya zakudya zimene anthu ambiri otchuka amanena kuti n’zabwino koma zili zowononga thanzi lanu.