Mawu a M'munsi
a Bungwe lina lofufuza za ngozi zachilengedwe linanena kuti ngati kwachitika chivomezi chomwe chapha anthu oposa 10, chakhudza anthu oposa 100, ngati boma lapempha kuti mayiko ena alithandize kapena ngati layamba kugwiritsa ntchito malamulo amphamvu pofuna kuthandiza anthu, ndiye kuti chimenecho ndi chivomezi champhamvu kwambiri.—Centre for Research on the Epidemiology of Disasters.