Mawu a M'munsi b Kuti mupeze malangizo ena othandiza pa nkhani ya zakudya komanso masewera olimbitsa thupi, werengani mutu 10, m’buku lakuti, Questions Young People Ask—Answers That Work, Volume 1, lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.