Mawu a M'munsi
a Baibulo sililimbikitsa kuchitira ana nkhanza kapena kuwalalatira. (Aefeso 4:29, 31; 6:4) Cholinga choperekera chilango ndi kuphunzitsa mwana ndipo makolo asamapereke chilango pongofuna kuphwetsa mkwiyo wawo.