Mawu a M'munsi
f Yesaya 9:6, 7; Luka 1:30-32. M’buku la Mateyu chaputala 1 muli m’ndandanda wa mayina a makolo a Yosefe, omwe anali bambo ake a Yesu, ndipo m’buku la Luka chaputala 3 muli m’ndandanda wa mayina a makolo a Mariya.