Mawu a M'munsi a Munthu amene amadzivulaza amadzipweteka yekha mwadala kaya kudzicheka, kudzimenya kapena kudzivulaza mwanjira ina.