Mawu a M'munsi
a Chifukwa chakuti Adamu ndi Hava sanamvere Mulungu, panayambikanso nkhani zikuluzikulu zokhudza Mulungu. Nkhani zimenezi zingatithandizenso kumvetsa chifukwa chimene Mulungu walolera kuti anthu azivutika. Kuti mudziwe zambiri werengani buku lakuti Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? pa webusaiti ya www.pr418.com/ny.