Mawu a M'munsi
a Buku lakuti, Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? muli mutu wakuti: “Kodi Zoona Zenizeni za Mulungu N’zotani?” ndi wakuti “Kodi Yesu Kristu Ndani?” Kuti mupeze bukuli mukhoza kupempha aliyense wa Mboni za Yehova kapena mukhoza kuliwerenga pa webusaiti ya www.pr418.com.