Mawu a M'munsi
a Li ndi muyezo umene anthu a ku China ankagwiritsa ntchito kale kwambiri poyezera kutalika kwa zinthu. Muyezowu wakhala ukusinthasintha koma zikuoneka kuti m’nthawi ya Zheng He, ‘li’ imodzi inali muyezo wa mamita pafupifupi 500.