Mawu a M'munsi
b Matenda ena, monga chithokomiro komanso mankhwala ena angachititsenso kuti azimayi azimva kutentha. Ngati mumamva kutentha ndi bwino kutsimikizira kaye kuti simukumva kutenthako chifukwa cha zinthu zimenezi m’malo mofulumira kuganiza kuti mukuyamba kusiya kusamba.