Mawu a M'munsi
c Pofuna kuthandiza anthu amene ali ndi mavuto osiyanasiyana obwera chifukwa cha kusiya kusamba, madokotala amatha kuwapatsa mankhwala oti asamakhumudwekhumudwe komanso akhoza kuwalangiza zinthu zoyenera kudya. Magazini ya Galamukani! siisankhira anthu mankhwala.