Mawu a M'munsi
a Baibulo silinena kuti Mulungu ali ndi mkazi weniweni amene anabereka naye ana. Koma limati Yesu ndi “Mwana wa Mulungu” chifukwa choti Yesuyo analengedwa mwachindunji ndi Mulungu ndipo ali ndi makhalidwe ofanana ndi a Atate wake.