Mawu a M'munsi
a Anthu ambiri amakayikira ngati Constantine anayambadi Chikhristu ndi zolinga zabwino. Buku lina linanena kuti chifukwa china chimene anthu amakayikirira zolinga zake n’choti, “ankavomereza zikhulupiriro zachikunja ndipo anachita zimenezi mpaka chakumapeto kwa ulamuliro wake.”