Mawu a M'munsi
a Charles Darwin analemba m’buku lake lina kuti: “Kuti mtundu wa nyama usinthe n’kukhala mtundu wina, zimachitika pang’onopang’ono komanso umangosintha pang’ono. Sizingatheke kuti mtundu winawake wa nyama ungosintha kamodzin’kamodzi n’kukhala mtundu wina.”