Mawu a M'munsi
a Anthu a ku Roma sanali oyamba kumanga ngalande za madzi. Anthu a ku Siriya, Iguputo, India komanso Perisiya ankamanga ngalande za madzi, Aroma asanayambe kumanga ngalande zoterezi.