Mawu a M'munsi b Kuti mudziwe chifukwa chake Mulungu walola kuti mavuto azichitikabe komanso mmene adzawathetsere, werengani mutu 8 ndi 11 m’buku lakuti, Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.