Mawu a M'munsi
a Mawu akuti “Mesiya” ndiponso “Khristu” tanthauzo lake ndi limodzi. “Mesiya” ndi mawu ochokera ku Chiheberi pomwe “Khristu” ndi mawu ochokera ku Chigiriki.—Yohane 1:41.