Mawu a M'munsi
a Zinthu monga mikangano, ziwawa kapena kuzunzidwa, zimachititsa anthu ena kuchoka panyumba pawo. Anthu oterewa amasowa pokhala m’dziko lawo lomwelo kapena m’dziko limene asamukira. Vuto limeneli lafotokozedwa mu Galamukani! ya February 8, 2002.