Mawu a M'munsi
b Anthu ena amafuna kugwira ntchito, koma amalephera chifukwa cha kulumala, matenda kapena ukalamba. Mulungu sadana ndi anthu oterewa koma amadana ndi amene ‘safuna kugwira ntchito.’—2 Atesalonika 3:10.