Mawu a M'munsi
a M’masamu a masiku ano a algebra, manambala amene sakudziwika amaimiridwa ndi x, y kapena zilembo zina. Mwachitsanzo akalemba kuti x + 4 = 6. Tikafuna kudziwa kuti x akuimira chiyani, timapanga 6 - 4 n’kupeza 2. Choncho x akuimira 2.