Mawu a M'munsi
a Kale Mulungu ankalola Aisiraeli kumenya nkhondo kuti asalandidwe malo awo. (2 Mbiri 20:15, 17) Koma zimenezi zinatha pamene anathetsa pangano lomwe anachita ndi Aisiraeli n’kukhazikitsa mpingo wachikhristu womwe anthu ake amapezeka padziko lonse.