Mawu a M'munsi
e Bungwe lina loona za umoyo ku Australia linalemba mavuto amene amabwera ngati munthu waikidwa magazi. Linati: “Munthu akaikidwa magazi, ndiye kuti waikidwa chiwalo chinachake. Ndiyeno munthu akaikidwa chiwalo china, thupi limadabwa ndipo limafuna chitachoka. Choncho kuikidwa magazi kuli ndi mavuto ake.”