Mawu a M'munsi
a Kuti mudziwe chifukwa chake Mulungu amalola kuti tizivutika, onani mutu 11 m’buku lakuti, Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? Bukuli ndi lofalitsidwa ndi a Mboni za Yehova ndipo likupezekanso pa webusaiti yathu ya www.jw.org/ny