Mawu a M'munsi
a Komanso Baibulo siligwirizana ndi zimene asayansi ena amanena zoti Mulungu analenga dzikoli m’masiku 6 enieni a maola 24. Kuti mudziwe zambiri, onani samba 24 mpaka 27 m’kabuku kachingelezi kakuti, Was Life Created? Kabukuka ndi kofalitsidwa ndi Mboni za Yehova. Mungapangenso dawunilodi kabukuka kwaulere pa webusaiti yathu ya www.pr418.com.