Mawu a M'munsi
b Achinyamata ambiri omwe ali kukoleji ku United States amakumana ndi mavuto ngati amenewa. Mwachitsanzo, lipoti la m’nyuzipepala ina linanena kuti achinyamata ambiri akamamaliza maphunziro awo amakhala ali ndi ngongole ya ndalama pafupifupi madola 33,000.—The Wall Street Journal.