Mawu a M'munsi
b Asayansi anapeza kuti nsomba za right whale zilipo za mitundu itatu. Mitundu imeneyi ndi Eubalaena australis, Eubalaena glacialis komanso Eubalaena japonica. Nsomba za mtundu wa Eubalaena australis zimapezeka kum’mwera kwa dziko lapansi. Pomwe zamitundu inayo zimapezeka kumpoto kwa dziko lapansi.