Mawu a M'munsi
b Mawu akuti “dziko lapansi latsopano” sakutanthauza kuti Mulungu adzalenganso dziko lina. Koma amatanthauza anthu omvera omwe azidzakhala padzikoli.—Salimo 66:4.