Mawu a M'munsi
c Baibulo limanena kuti Mulungu anasankha anthu ochepa okha kuti adzapite kumwamba. Anthuwa ndi okwana 144,000 ndipo azidzalamulira dzikoli limodzi ndi Yesu ali kumwamba.—1 Petulo 1:3, 4; Chivumbulutso 14:1.