Mawu a M'munsi a Mfundo zina za m’Baibulo zothandiza pa nkhani ya kuthetsa kusamvana zikupezeka pa Mateyu 5:23, 24; 18:15-17.