Mawu a M'munsi
b Ngati mukulerabe ana, musamaiwale kuti ndinu “thupi limodzi” ndi mwamuna kapena mkazi wanu. (Maliko 10:8) Nawonso ana amamva kuti ndi otetezeka akaona kuti makolo awo amakondana kwambiri.