Mawu a M'munsi
a Poyamba anthu a ku Europe sankamvetsa kuti diso limagwira ntchito mofanana ndi kachipinda kam’dima kaja. Anthuwa anayamba kuzimvetsa bwino cha m’ma 1600, katswiri wina dzina lake Johannes Kepler atafotokoza zimene zimachitika.