Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO

Mawu a M'munsi

b Ngakhale kuti nyenyezi 7 zimene zili m’dzanja lamanja la Yesu zikuimira oyang’anira odzozedwa a mumpingo wachikhristu, akulu ambiri m’mipingo yoposa 100,000 padziko lonse ali m’gulu la khamu lalikulu. (Chivumbulutso 1:16; 7:9) Kodi iwo ali ndi udindo wotani? Akuluwa amaikidwa ndi mzimu woyera kudzera mwa Akhristu odzozedwa, omwe ndi kapolo wokhulupirika ndi wanzeru. Motero, tinganene kuti akuluwa akutsogoleredwa ndi dzanja lamanja la Yesu chifukwa iwonso ndi abusa ake aang’ono. (Yesaya 61:5, 6; Machitidwe 20:28) Iwo amathandiza “nyenyezi 7” chifukwa amatumikira kumene kulibe abale odzozedwa oyenerera.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena