Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO

Mawu a M'munsi

b William L. Shirer analemba m’buku lake lofotokoza mbiri yakale kuti von Papen, “ndi amene anathandiza kwambiri Hitler kukhala wolamulira kuposa munthu wina aliyense m’dziko la Germany.” (The Rise and Fall of the Third Reich) Mu January 1933, von Schleicher, amene kale anali wolamulira wa dziko la Germany, anati von Papen “anali munthu wachinyengo kwambiri, moti Yudasi Isikariyoti angaoneke ngati munthu wabwino poyerekezera ndi iyeyo.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena