Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO

Mawu a M'munsi

c Anthu amakhulupirira kuti Papias wa ku Herapoli, anaphunzitsidwa mfundo zina za m’Baibulo ndi ophunzira a Yohane, yemwe analemba buku la Chivumbulutso. N’zochititsa chidwi kuti Eusebius, wolemba mbiri yakale wa m’zaka za m’ma 300 C.E., ananena kuti Papias ankakhulupirira kuti Khristu adzalamulira kwa zaka 1,000 zenizeni (ngakhale kuti Eusebius ankamutsutsa kwambiri pa mfundo imeneyi).—The History of the Church, Eusebius, III, 39.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena