Mawu a M'munsi
b Sitikunena za mikhalidwe imene mwana amafunikira kutetezeredwa kwa kholo lake lankhanza. Ndiponso, ngati kholo linalo limayesa kufooketsa ulamuliro wanu, mwinamwake pofuna kunyengerera ana kuti akusiyeni, kungakhale bwino kulankhula ndi mabwenzi odziƔa zambiri, monga akulu mumpingo wachikristu, kuti akupatseni uphungu wa mmene mungachitire ndi mkhalidwewo.