Mawu a M'munsi
a Mawu akuti “milomo yodetsedwa” ndi oyenera, chifukwa nthawi zambiri m’Baibulo mawu akuti milomo amagwiritsidwa ntchito mophiphiritsa potanthauza zolankhula kapena chilankhulo. Machimo ambiri amene anthu ochimwafe timachita amachokera pa zimene timalankhula.—Miyambo 10:19; Yakobo 3:2, 6.