Mawu a M'munsi
b Yehova amatchedwa Atate chifukwa ndi Mlengi. (Yesaya 64:8) Yesu amatchulidwa kuti ndi Mwana wa Mulungu chifukwa analengedwa ndi Mulungu. N’chifukwa chakenso angelo komanso Adamu amatchulidwa kuti ndi ana a Mulungu.—Yobu 1:6; Luka 3:38.