Mawu a M'munsi
a Kuchokera mu October 607 B.C.E. kufika mu October 1 B.C.E. panadutsa zaka 606. Kuchokera mu October 1 B.C.E. kudzafika mu October 1914 C.E. panadutsa zaka 1,914. Tikaphatikiza zaka 606 ndi zaka 1,914, timapeza zaka 2,520. Kuti mumve zambiri zokhudza kugonjetsedwa kwa Yerusalemu mu 607 B.C.E., onani buku lakuti Kukambitsirana za m’Malemba, tsamba 231-233, lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.