Mawu a M'munsi
c M’Malemba, mawu akuti “zinthu zodetsa” amatanthauza machimo osiyanasiyana. Sikuti zodetsa zilizonse zimafunikira komiti ya chiweruzo, komabe munthu angathe kuchotsedwa mumpingo ngati akupitirizabe kuchita zonyansa.—2 Akorinto 12:21; Aefeso 4:19; onani “Mafunso Ochokera kwa Owerenga” mu Nsanja ya Olonda ya July 15, 2006.