Mawu a M'munsi
b Baibulo komanso mabuku a mbiri yakale amasonyeza kuti Yesu ayenera kuti anabadwa mu 2 B.C.E., m’mwezi wa Etanimu pa kalendala yachiyuda. Pa kalendala yathu mwezi umenewo ndi mwezi wa September kapena October. Onani buku la Insight on the Scriptures, Voliyumu 2, patsamba 56 ndi 57, lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.